Genesis 2:18 - Buku Lopatulika18 Yehova Mulungu ndipo anati, Si kwabwino kuti munthu akhale yekha; ndidzampangira womthangatira iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Yehova Mulungu ndipo anati, Si kwabwino kuti munthu akhale yekha; ndidzampangira womthangatira iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pambuyo pake Chauta adati, “Sibwino kuti munthuyu akhale yekha. Ndipanga mnzake woti azimthandiza.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndipo Yehova Mulungu anati, “Sibwino kuti munthu akhale yekha. Ndidzamupangira mnzake womuthandiza.” Onani mutuwo |