Genesis 2:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Yehova Mulungu anamuuza munthuyo, nati, Mitengo yonse ya m'munda udyeko; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Yehova Mulungu anamuuza munthuyo, nati, Mitengo yonse ya m'munda udyeko; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ndipo Chauta adamlamula munthuyo kuti, “Uzidya zipatso za mtengo uliwonse wam'mundawu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndipo Yehova Mulungu analamula munthu uja kuti, “Uzidya zipatso za mu mtengo wina uliwonse mʼmundamu; Onani mutuwo |