Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 2:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo Yehova Mulungu anatenga munthuyo, namuika iye m'munda wa Edeni kuti aulime nauyang'anire.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo Yehova Mulungu anatenga munthuyo, namuika iye m'munda wa Edeni kuti aulime nauyang'anire.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Tsono Chauta adamtenga munthuyo, namukhazika m'munda wa Edeni uja kuti azilima ndi kumausamala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Yehova Mulungu anatenga munthu uja ndi kumuyika mʼmunda wa Edeni kuti awulime ndi kuwusamalira.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 2:15
7 Mawu Ofanana  

Dzina la mtsinje wachitatu ndi Tigrisi: umenewo ndiwo wakuyenda cha kum'mawa kwake kwa Asiriya. Mtsinje wachinai ndi Yufurate.


Ndipo Yehova Mulungu anamuuza munthuyo, nati, Mitengo yonse ya m'munda udyeko;


Tsiku lachisanu ndi chiwiri Mulungu anamaliza ntchito yonse anaipanga; ndipo anapuma tsiku lachisanu ndi chiwiri ku ntchito yake yonse.


Ndipo Yehova Mulungu anabzala m'munda ku Edeni chakum'mawa; momwemo ndipo adaika munthu adamuumbayo.


Ngati ndakwirira zolakwa zanga monga Adamu, ndi kubisa mphulupulu yanga m'chifuwa mwanga;


Pakuti udzadya za ntchito ya manja ako; wodala iwe, ndipo kudzakukomera.


Wakubayo asabenso; koma makamaka agwiritse ntchito, nagwire ntchito yokoma ndi manja ake, kuti akhale nacho chakuchereza wosowa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa