Genesis 2:11 - Buku Lopatulika11 Dzina la woyamba ndi Pisoni: umenewo ndiwo wozungulira dziko lonse la Havila, m'mene muli golide; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Dzina la wakuyamba Pisoni: umenewo ndiwo wozungulira dziko lonse la Havila, m'mene muli golide; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mtsinje woyamba ndi Pisoni, ndipo umayenda mozungulira dziko la Havila, kumene kumapezeka golide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Dzina la mtsinje woyamba ndi Pisoni; uwu umazungulira dziko lonse la Havila, kumene kuli golide. Onani mutuwo |