Genesis 2:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo unatuluka mu Edeni mtsinje wakuthirira m'mundamo, m'menemo ndipo unalekana nuchita miyendo inai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo unatuluka m'Edeni mtsinje wakuthirira m'mundamo, m'menemo ndipo unalekana nuchita miyendo inai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mtsinje wotuluka mu Edeni momwemo, unkayenda numathirira mundawo. Mtsinjewo udagaŵika panai, nusanduka mitsinje inai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mtsinje wothirira mundawo unkatuluka mu Edeni; kuchokera apo unkagawikana kukhala mitsinje inayi. Onani mutuwo |