Genesis 19:28 - Buku Lopatulika28 ndipo anayang'anira ku Sodomu ndi ku Gomora ndi ku dziko lonse la chigwa, ndipo anapenya, taonanitu, utsi wa dzikolo unakwera, monga utsi wa ng'anjo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 ndipo anayang'anira ku Sodomu ndi ku Gomora ndi ku dziko lonse la chigwa, ndipo anapenya, taonanitu, utsi wa dzikolo unakwera, monga utsi wa ng'anjo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Adayang'ana ku mizinda ya Sodomu ndi Gomora ndi ku chigwa chija. Ndipo adangoona utsi uli tolotolo kutuluka m'chigwamo ngati utsi wotuluka m'ng'anjo ya moto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Anayangʼana kumunsi ku Sodomu, Gomora ndi ku dziko lonse la ku chigwa, ndipo anaona chiwutsi chikufuka mʼdzikolo ngati chikuchokera mʼngʼanjo. Onani mutuwo |