Genesis 19:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo Abrahamu analawira m'mamawa kunka kumalo kumene anaima pamaso pa Yehova: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo Abrahamu analawira m'mamawa kunka kumalo kumene anaima pamaso pa Yehova: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 M'maŵa mwake, m'mamaŵa, Abrahamu adathamangira ku malo omwe aja, kumene adaaimirira pamaso pa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Mmawa mwake, Abrahamu ananyamuka nabwerera kumalo kumene anakumana ndi Yehova kuja. Onani mutuwo |