Genesis 19:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo dzuwa lidakwera padziko pamene Loti anafika ku Zowari. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo dzuwa lidakwera pa dziko pamene Loti anafika ku Zowari. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Pamene dzuŵa linkatuluka, Loti nkuti atafika kale ku Zowari. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pamene Loti amafika ku Zowari, nʼkuti dzuwa litatuluka. Onani mutuwo |