Genesis 19:22 - Buku Lopatulika22 Fulumira, thawira kumeneko; pakuti sindithai kuchita kanthu usadafike kumeneko. Chifukwa chake anatcha dzina la mzindawo Zowari. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Fulumira, thawira kumeneko; pakuti sindithai kuchita kanthu usadafike kumeneko. Chifukwa chake anatcha dzina la mudziwo Zowari. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Fulumira! Thamanga! Sindichita kena kalikonse mpaka iwe utafika kumeneko.” Choncho Loti adathamanga nakafika ku kamzinda kaja. Nchifukwa chake kamzindako adakatcha Zowari. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Koma uthawireko mofulumira chifukwa sindichita kena kalikonse mpaka utafikako.” (Nʼchifukwa chake mudziwo unatchedwa Zowari). Onani mutuwo |