Genesis 19:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anati kwa iye, Taona, ndikuvomereza iwe pamenepanso kuti sindidzaononga mzinda uwu umene wandiuza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anati kwa iye, Taona, ndikuvomereza iwe pamenepanso kuti sindidzaononga mudzi uwu umene wandiuza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Munthuyo adayankha kuti, “Zimenezo ndavomereza. Kamzinda kameneko sindikaononga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Mngeloyo anati kwa iye, “Chabwino, ndavomeranso pempho lako, sindiwononga mudzi ukunenawo. Onani mutuwo |