Genesis 18:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo anthuwo anatembenuka nachoka kumeneko, napita kunka ku Sodomu. Koma Abrahamu anaimabe pamaso pa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo anthuwo anatembenuka nachoka kumeneko, napita kunka ku Sodomu. Koma Abrahamu anaimabe pamaso pa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Anthu aja adachoka, napita ku Sodomu, koma Abrahamu adatsarira ndi Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Anthu aja anatembenuka nʼkumapita, kulowera ku Sodomu, koma Abrahamu anali chiyimirire pamaso pa Yehova. Onani mutuwo |