Genesis 18:21 - Buku Lopatulika21 ndidzatsikatu ndikaone ngati anachita monse monga kulira kwake kumene kunandifikira: ngati sanatero ndidzadziwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 ndidzatsikatu ndikaone ngati anachita monse monga kulira kwake kumene kunandifikira: ngati sanatero ndidzadziwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Choncho ndikuti nditsikireko kuti ndikaone ngati zolakwa zimene ndamvazo ndi zoona. Ngati si choncho, ndidzadziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 choncho ndikuti ndipiteko ndikaone ngati zimene achita zilidi zoyipa monga mmene madandawulo andipezera Ine. Ngati sizili choncho, ndikadziwa.” Onani mutuwo |