Genesis 18:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anthuwo anauka kuchokera kumeneko nayang'ana ku Sodomu; ndipo Abrahamu ananka nao kuwaperekeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anthuwo anauka kuchokera kumeneko nayang'ana ku Sodomu; ndipo Abrahamu ananka nao kuwaperekeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono anthuwo adachoka, nafika pamalo pamene anali kupenya Sodomu. Abrahamu adapita nawo limodzi, naŵalozera njira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Kenaka anthu aja ananyamuka ndi kumapita, molunjika ku Sodomu. Ndipo Abrahamu anayenda nawo pamodzi kuwaperekeza. Onani mutuwo |