Genesis 18:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Yehova adati, Kodi ndidzabisira Abrahamu chimene ndichita? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Yehova adati, Kodi ndidzabisira Abrahamu chimene ndichita? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Ndipo Chauta adanena mwa Iye yekha kuti, “Abrahamuyu sindingamubisire chomwe ndikuti ndichite. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Tsono Yehova anati mu mtima mwake, “Kodi ndingamubisire Abrahamu chimene ndikuti ndichite posachedwa? Onani mutuwo |