Genesis 18:15 - Buku Lopatulika15 Koma Sara anakana, nati, Sindinasekai; chifukwa anaopa. Ndipo anati, Iai; koma unaseka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Koma Sara anakana, nati, Sindinasekai; chifukwa anaopa. Ndipo anati, Iai; koma unaseka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Apo Sara adakana chifukwa cha mantha, adati, “Sindidaseke.” Koma Iye adati, “Inde, unaseka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Koma Sara ndi mantha ananama nati, “Sindinaseke.” Koma Iye anati, “Inde iwe unaseka.” Onani mutuwo |