Genesis 18:11 - Buku Lopatulika11 Koma Abrahamu ndi Sara anali okalamba, anapitirira masiku ao; ndipo kunaleka kwa Sara konga kumachita ndi akazi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma Abrahamu ndi Sara anali okalamba, anapitirira masiku ao; ndipo kunaleka kwa Sara konga kumachita ndi akazi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Abrahamu pamodzi ndi Sara anali nkhalamba zokhazokha, ndipo nthaŵi imeneyo nkuti Sara ataleka kusamba monga amachitira akazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Abrahamu ndi Sara anali okalamba kale ndipo anali ndi zaka zambiri. Sara nʼkuti atapyola kale pa msinkhu oti nʼkubereka. Onani mutuwo |