Genesis 17:26 - Buku Lopatulika26 Tsiku lomwelo anadulidwa Abrahamu ndi Ismaele mwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Tsiku lomwelo anadulidwa Abrahamu ndi Ismaele mwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Pa tsiku limeneli Abrahamu ndi mwana wake Ismaele adaumbalidwa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Onse, Abrahamu ndi mwana wake Ismaeli, anachita mdulidwe tsiku limodzi. Onani mutuwo |