Genesis 17:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Ismaele mwana wake anali wa zaka khumi ndi zitatu pamene anadulidwa m'khungu lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Ismaele mwana wake anali wa zaka khumi ndi zitatu pamene anadulidwa m'khungu lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Mwana wake Ismaele anali wa zaka 13 pamene adaumbalidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 ndipo mwana wake Ismaeli anali ndi zaka khumi ndi zitatu; Onani mutuwo |