Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 17:27 - Buku Lopatulika

27 Ndipo amuna onse a m'nyumba mwake obadwa m'nyumba, ndi ogulidwa ndi ndalama kwa alendo, anadulidwa pamodzi naye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Ndipo amuna onse a m'nyumba mwake obadwa m'nyumba, ndi ogulidwa ndi ndalama kwa alendo, anadulidwa pamodzi naye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 pamodzi ndi anthu aamuna onse, amuna obadwira m'banja mwake ndiponso ena amene adaŵagula ndi ndalama kwa alendo, onsewo adaumbalidwa pamodzi ndi iyeyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Aliyense wamwamuna wa pa banja pa Abrahamu, kuphatikizapo iwo amene anabadwira pa banja pomwepo kapena akapolo ogula ndi ndalama kwa alendo, anachita mdulidwe.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 17:27
4 Mawu Ofanana  

Pamene anamva Abramu kuti mphwake anagwidwa, anatuluka natsogolera anyamata ake opangika, obadwa kunyumba kwake, mazana atatu kudza khumi ndi asanu ndi atatu, nawalondola kufikira ku Dani.


Ili ndi pangano langa limene uzisunga pakati pa Ine ndi iwe ndi mbeu zako za pambuyo pako: azidulidwa amuna onse a mwa inu.


Tsiku lomwelo anadulidwa Abrahamu ndi Ismaele mwana wake.


Chifukwa ndamdziwa iye kuti alamulire ana ake ndi banja lake la pambuyo pake, kuti asunge njira ya Yehova, kuchita chilungamo ndi chiweruziro, kuti Yehova akamtengere Abrahamu chomwe anamnenera iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa