Genesis 16:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo mthenga wa Yehova anati kwa iye, Taona, uli ndi pakati, ndipo udzabala mwana wamwamuna; nudzamutcha dzina lake Ismaele; chifukwa Yehova anamva kusauka kwako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo mthenga wa Yehova anati kwa iye, Taona, uli ndi pakati, ndipo udzabala mwana wamwamuna; nudzamutcha dzina lake Ismaele; chifukwa Yehova anamva kusauka kwako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Popitiriza mau mngeloyo adati, “Tsopano uli pafupi kukhala ndi mwana wamwamuna, udzamutche Ismaele, ndiye kuti Chauta wamva kulira kwako pa zovuta zako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mngelo wa Yehova uja anamuwuzanso kuti, “Ndiwe woyembekezera ndipo udzabala mwana wamwamuna. Udzamutcha dzina lake Ismaeli, pakuti Yehova wamva kulira chifukwa cha kuzunzika kwako. Onani mutuwo |