Genesis 16:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo mthenga wa Yehova anati kwa iye, Ndidzachulukitsa ndithu mbeu zako, kuti unyinji wao sudzawerengeka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo mthenga wa Yehova anati kwa iye, Ndidzachulukitsa ndithu mbeu zako, kuti unyinji wao sudzawerengeka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ndidzakupatsa zidzukulu zochuluka, zosaŵerengeka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndidzakupatsa zidzukulu zambiri zoti munthu sangaziwerenge.” Onani mutuwo |