Genesis 15:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo panali pamene litalowa dzuwa ndi kudza mdima, taonani, ng'anjo yofuka utsi ndi muuni wamoto unadutsa pakati pa mabanduwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo panali pamene litalowa dzuwa ndi kudza mdima, taonani, ng'anjo yofuka utsi ndi muuni wamoto wapita pakati pa mabanduwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Dzuŵa litangoloŵa, kachisisira katagwa, mwadzidzidzi padaoneka mphika wogaduka ndi moto, pamodzi ndi nsakali yoyaka, ndipo ziŵirizi zidadutsa pakati pa nyama zodulidwa zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Dzuwa litalowa ndipo mdima utagwa, panaoneka mʼphika wofuka nthunzi ya moto ndi sakali yoyaka ndipo zinadutsa pakati pa zidutswa za nyama zija. Onani mutuwo |