Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 14:9 - Buku Lopatulika

9 ndi Kedorilaomere mfumu ya Elamu, ndi Tidala mfumu ya Goimu, ndi Amurafere mfumu ya Sinara, ndi Ariyoki mfumu ya Elasara; mafumu anai kumenyana ndi asanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 ndi Kedorilaomere mfumu ya Elamu, ndi Tidala mfumu ya Goimu, ndi Amurafere mfumu ya Sinara, ndi Ariyoki mfumu ya Elasara; mafumu anai kugwirana ndi asanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 ndi Kedorilaomere wa ku Elamu, Tidala wa ku Goimu, Amurafere wa ku Sinara ndi Ariyoki wa ku Elasara, mafumu asanu kulimbana ndi mafumu anai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Kedorilaomere mfumu ya Elamu, Tidala mfumu ya Goimu, Amarafeli mfumu ya Sinara ndi Arioki mfumu ya Elasara. Mafumu anayi analimbana ndi mafumu asanu.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 14:9
5 Mawu Ofanana  

Ana aamuna a Semu; Elamu, ndi Asiriya, ndi Aripakisadi, ndi Ludi, ndi Aramu.


Ndipo panali masiku a Amurafere mfumu ya Sinara, ndi Ariyoki mfumu ya Elasara, ndi Kedorilaomere mfumu ya Elamu, ndi Tidala mfumu ya Goimu,


Chigwa cha Sidimu chinali ndi zitengetenge thoo; ndipo anathawa mafumu a ku Sodomu ndi Gomora nagwa m'menemo: amene anatsala anathawira kuphiri.


Ndipo anatuluka mfumu ya Sodomu, ndi ya Gomora, ndi mfumu ya Adima, ndi mfumu ya Zeboimu, ndi mfumu ya Bela (kumeneko ndi ku Zowari) ndipo anawathira nkhondo m'chigwa cha Sidimu;


Mau a Yehova amene anafika kwa Yeremiya mneneri, onena za Elamu poyamba kulamulira Zedekiya mfumu ya Yuda, kuti,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa