Genesis 14:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anatuluka mfumu ya Sodomu, ndi ya Gomora, ndi mfumu ya Adima, ndi mfumu ya Zeboimu, ndi mfumu ya Bela (kumeneko ndi ku Zowari) ndipo anawathira nkhondo m'chigwa cha Sidimu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anatuluka mfumu ya Sodomu, ndi ya Gomora, ndi mfumu ya Adima, ndi mfumu ya Zeboimu, ndi mfumu ya Bela (kumeneko ndi ku Zowari) ndipo anawathira nkhondo m'chigwa cha Sidimu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono mafumu a ku Sodomu, Gomora, Adima, Zeboimu ndi Bela adasonkhanitsa ankhondo ao m'chigwa cha Sidimu, nalimbana Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tsono mafumu a ku Sodomu, Gomora, Adima, Zeboimu ndi ku Bela (ku Zowari) anapita ku Chigwa cha Sidimu kukakonzekera kuthira nkhondo Onani mutuwo |