Genesis 14:6 - Buku Lopatulika6 ndi Ahori paphiri lao Seiri kufikira ku Eliparani, kumene kuli m'mbali mwa chipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 ndi Ahori pa phiri lao Seiri kufikira ku Eliparani, kumene kuli m'mbali mwa chipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adagonjetsanso Ahori amene ankakhala m'mapiri a Seiri mpaka ku Eliparani ku malire a chipululu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 amene ankakhala ku Ahori, ku dziko la mapiri la Seiri mpaka ku Eli Parani kufupi ndi chipululu. Onani mutuwo |