Genesis 14:4 - Buku Lopatulika4 Zaka khumi ndi ziwiri iwo anamtumikira Kedorilaomere, chaka chakhumi ndi chitatu anapanduka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Zaka khumi ndi ziwiri iwo anamtumikira Kedorilaomere, chaka chakhumi ndi chitatu anapanduka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Kedorilaomere ndiye ankalamulira onseŵa pa zaka khumi ndi ziŵiri, koma chaka chakhumi ndi chitatu onseŵa adamuukira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kwa zaka khumi ndi ziwiri anali pansi pa ulamuliro wa Kedorilaomere, koma mʼchaka cha khumi ndi chitatu anamuwukira. Onani mutuwo |