Genesis 14:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anatenga chuma chonse cha Sodomu ndi Gomora ndi zakudya zao zonse, namuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anatenga chuma chonse cha Sodomu ndi Gomora ndi zakudya zao zonse, namuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mafumu anai aja adatenga zonse za ku Sodomu ndi za ku Gomora, pamodzi ndi chakudya, nachokapo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mafumu anayi aja anatenga katundu yense ndi chakudya chonse cha ku Sodomu ndi Gomora napita nazo. Onani mutuwo |