Genesis 14:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anagwira Loti mwana wa Abramu amene anakhala mu Sodomu, ndi chuma chake, namuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anagwira Loti mwana wa Abramu amene anakhala m'Sodomu, ndi chuma chake, namuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Adamtenganso Loti, mphwake wa Abramu uja, pamodzi ndi zake zonse, chifukwa ankakhala ku Sodomu komweko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Anatenganso Loti, mwana wa mʼbale wake wa Abramu pamodzi ndi katundu wake popeza ankakhala mu Sodomu. Onani mutuwo |