Genesis 11:25 - Buku Lopatulika25 ndipo Nahori anakhala ndi moyo zaka zana limodzi kudza khumi ndi zisanu ndi zinai, atabala Tera, nabala ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 ndipo Nahori anakhala ndi moyo zaka zana limodzi kudza khumi ndi zisanu ndi zinai, atabala Tera, nabala ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pambuyo pake adakhala ndi moyo zaka 119, ndipo adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Atabereka Tera, Nahori anakhala ndi moyo zaka zina 119 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwo |