Genesis 11:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo Tera anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi awiri, nabala Abramu, ndi Nahori ndi Harani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo Tera anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi awiri, nabala Abramu, ndi Nahori ndi Harani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Tera ali wa zaka 70, adabereka Abramu, Nahori ndi Harani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Pamene Tera anali ndi zaka 70, anabereka Abramu, Nahori ndi Harani. Onani mutuwo |