Genesis 11:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo Nahori anakhala ndi moyo zaka makumi awiri kudza zisanu ndi zinai, nabala Tera: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo Nahori anakhala ndi moyo zaka makumi awiri kudza zisanu ndi zinai, nabala Tera: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Nahori ali wa zaka 29, adabereka mwana dzina lake Tera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Pamene Nahori anali ndi zaka 29, anabereka Tera. Onani mutuwo |