Genesis 11:21 - Buku Lopatulika21 ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi ziwiri, atabala Serugi, nabala ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi ziwiri, atabala Serugi, nabala ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pambuyo pake adakhala ndi moyo zaka zina 207, ndipo adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Atabereka Serugi, Reu anakhala ndi moyo zaka zina 207 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwo |