Genesis 11:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Serugi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Nahori: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Serugi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Nahori: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Serugi ali wa zaka 30, adabereka mwana dzina lake Nahori. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Pamene Serugi anali ndi zaka makumi atatu, anabereka Nahori. Onani mutuwo |