Genesis 11:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza ziwiri, nabala Serugi: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza ziwiri, nabala Serugi: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Reu ali wa zaka 32, adabereka mwana dzina lake Serugi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Pamene Reu anali ndi zaka 32, anabereka Serugi. Onani mutuwo |