Genesis 11:19 - Buku Lopatulika19 ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi zinai, atabala Reu, nabala ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi zinai, atabala Reu, nabala ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Pambuyo pake adakhala ndi moyo zaka zina 209, ndipo adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Atabereka Reu, Pelegi anakhala zaka zina 209 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwo |