Genesis 11:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Reu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Reu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pelegi ali wa zaka 30 adabereka mwana dzina lake Reu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pamene Pelegi anali ndi zaka makumi atatu, anabereka Reu. Onani mutuwo |