Genesis 11:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Sela anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Eberi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Sela anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Eberi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pamene Sela anali wa zaka 30, adabereka mwana dzina lake Eberi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Pamene Sela anali ndi zaka makumi atatu, anabereka Eberi. Onani mutuwo |