Genesis 11:13 - Buku Lopatulika13 ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza zitatu, atabala Sela, nabala ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza zitatu, atabala Sela, nabala ana aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Pambuyo pake adakhala ndi moyo zaka zina 403, ndipo adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Atabereka Sela, Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka zina 403 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwo |