Genesis 11:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza zisanu nabala Sela; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza zisanu nabala Sela; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pamene Aripakisadi anali wa zaka 35, adabereka mwana dzina lake Sela. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pamene Aripakisadi anali ndi zaka 35, anabereka Sela. Onani mutuwo |