Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 10:7 - Buku Lopatulika

7 Ndi ana aamuna a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Raama, ndi Sabiteka; ndi ana a Raama: Sheba ndi Dedani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndi ana amuna a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Raama, ndi Sabiteka; ndi ana a Raama: Sheba ndi Dedani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ana a Kusi anali Seba, Havila, Sabita, Raama ndi Sabiteka. Ana a Raama anali Sheba ndi Dedani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ana aamuna a Kusi anali: Seba, Havila, Sabita, Raama ndi Sabiteka. Ana aamuna a Raama anali: Seba ndi Dedani.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 10:7
11 Mawu Ofanana  

Ndipo Kusi anabala Nimirodi; ndipo iye anayamba kukhala wamphamvu padziko lapansi.


Dzina la woyamba ndi Pisoni: umenewo ndiwo wozungulira dziko lonse la Havila, m'mene muli golide;


Ndipo atamva mfumu yaikazi ya ku Sheba mbiri ya Solomoni yakubukitsa dzina la Yehova, anadza kumuyesera iye ndi miyambi yododometsa.


Ndi ana a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Raama, ndi Sabiteka. Ndi ana a Raama: Sheba, ndi Dedani.


koma anazigwera Aseba, nazitenga, nawapha anyamata ndi lupanga lakuthwa, ndipo ndapulumuka ine ndekha kudzakuuzani.


Mafumu a ku Tarisisi ndi ku Zisumbuzo adzabwera nacho chopereka; mafumu a ku Sheba ndi Seba adzadza nazo mphatso.


Katundu wa pa Arabiya. M'nkhalango ya mu Arabiya mudzagona, inu makamu oyendayenda a Dedani.


Chifukwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wako, Woyera wa Israele, Mpulumutsi wako; ndapatsa Ejipito dombolo lako, Etiopiya ndi Seba m'malo mwako.


Anthu a ku Dedani anakutsatsa malonda, zisumbu zambiri zinazolowerana nawe malonda ako, anabwera nazo minyanga ndi phingo kugulana nawe malonda.


Dedani anagulana nawe malonda ndi nsalu za mtengo wake zoyenda nazo pa kavalo.


Amalonda a ku Sheba ndi a ku Raama anagulana nawe malonda; anagula malonda ako ndi zonunkhira zoposa zilizonse, ndi miyala iliyonse ya mtengo wake, ndi golide.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa