Genesis 10:31 - Buku Lopatulika31 Amenewa ndi ana a Semu, monga mwa mabanja ao, mwa zinenedwe zao, m'maiko ao, m'mitundu yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Amenewa ndi ana a Semu, monga mwa mabanja ao, mwa zinenedwe zao, m'maiko ao, m'mitundu yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Ameneŵa ndiwo zidzukulu za Semu. Mafuko ao anali osiyanasiyana, ndipo ankakhalanso m'maiko osiyanasiyana. Fuko lililonse linkalankhula chilankhulo chakechake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Amenewa ndiwo ana a Semu monga mwa mafuko ndi ziyankhulo zawo, mʼmadera omwe ankakhala ndi mitundu yawo. Onani mutuwo |