Genesis 10:30 - Buku Lopatulika30 Kwao kunayamba pa Mesa pakunka ku Sefari phiri la kum'mawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Kwao kunayamba pa Mesa pakunka ku Sefari phiri la kum'mawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Dziko limene ankakhalamo lidayambira ku Mesa kumaloŵa ku Sefari ku mapiri chakuvuma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Chigawo chimene ankakhala chinayambira ku Mesa mpaka ku Seferi, ku dera la mapiri chakummawa. Onani mutuwo |