Genesis 10:14 - Buku Lopatulika14 ndi Patirusimu, ndi Kasiluhimu, m'menemo ndipo anatuluka Afilisti, ndi Kafitori. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 ndi Patirusimu, ndi Kasiluhimu, m'menemo ndipo anatuluka Afilisti, ndi Kafitori. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Patirusi, Kasilu ndi Kafitori, makolo a Afilisti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Apaturusi, Akasilu ndi Akafitori (kumene kunachokera Afilisti). Onani mutuwo |