Genesis 10:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Kanani anabala Sidoni woyamba wake, ndi Heti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Kanani anabala Sidoni woyamba wake, ndi Heti: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Kanani adabereka mwana wake wachisamba dzina lake Sidoni, ndipo adaberekanso Heti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kanaani anabereka mwana wake wachisamba, Sidoni, ndipo anaberekanso Ahiti; Onani mutuwo |