Genesis 10:13 - Buku Lopatulika13 Ejipito ndipo anabala Ludimu, ndi Anamimu, ndi Lehabu, ndi Nafituhimu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ejipito ndipo anabala Ludimu, ndi Anamimu, ndi Lehabu, ndi Nafituhimu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ejipito ndi amene anali kholo la anthu a ku Ludi, Anamu, Lehabu, Nafutu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Igupto ndiye kholo la Aludi, Aanami, Alehabu, Anafutu, Onani mutuwo |