Genesis 10:12 - Buku Lopatulika12 ndi Reseni pakati pa Ninive ndi Kala: umenewo ndi mzinda waukulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 ndi Reseni pakati pa Ninive ndi Kala: umenewo ndi mudzi waukulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 ndi mzinda wa Reseni umene uli pakati pa Ninive ndi mzinda waukulu uja wa Kala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 ndi Reseni, mzinda waukulu umene uli pakati pa Ninive ndi Kala. Onani mutuwo |