Genesis 1:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Mulungu analitcha thambolo Kumwamba. Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachiwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Mulungu analitcha thambolo Kumwamba. Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachiwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Cholekanitsacho adachitcha dzina loti Thambo. Ndipo kudali madzulo ndiponso m'maŵa, tsiku lachiŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mulungu anatcha thambo lija “kumwamba.” Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku lachiwiri. Onani mutuwo |