Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 1:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Mulungu anatcha thambo lija “kumwamba.” Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku lachiwiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

8 Ndipo Mulungu analitcha thambolo Kumwamba. Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachiwiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo Mulungu analitcha thambolo Kumwamba. Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachiwiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Cholekanitsacho adachitcha dzina loti Thambo. Ndipo kudali madzulo ndiponso m'maŵa, tsiku lachiŵiri.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 1:8
11 Mawu Ofanana  

Mulungu anawutcha mtundawo “dziko,” madzi osonkhana pamodziwo anawatcha “nyanja.” Ndipo Mulungu anaona kuti zinali bwino.


Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku lachitatu.


Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku lachinayi.


Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku lachisanu.


Mulungu anaona zonse zimene anazilenga kuti zinali zabwino kwambiri. Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa, tsiku lachisanu ndi chimodzi.


Mulungu anatcha kuwalako “usana” ndipo mdima anawutcha “usiku.” Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku loyamba.


Ndipo Mulungu anapanga thambo nalekanitsa madzi amene anali pansi ndi pamwamba pa thambo lija, ndipo zinachitikadi.


Mulungu anati, “Madzi a pansi pa thambo asonkhane pa malo amodzi kuti mtunda uwoneke,” ndipo zinachitikadi.


Iye analenga mwamuna ndi mkazi. Anawadalitsa ndipo anawatcha “Munthu.”


Amene mwachidziwitso chake anapanga mayiko akumwamba, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.


Uthenga wa Yehova kwa Israeli. Yehova, amene amayala mlengalenga, amene amayika maziko a dziko lapansi, ndiponso amene amalenga mzimu wokhala mwa munthu, akunena kuti,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa