Genesis 1:18 - Buku Lopatulika18 zilamulire usana ndi usiku, zilekanitse kuyera ndi mdima: ndipo anaona Mulungu kuti kunali kwabwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Nizilamulire usana ndi usiku, nizilekanitse kuyera ndi mdima: ndipo anaona Mulungu kuti kunali kwabwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 kuti iziŵala usana ndi usiku, kulekanitsa kuyera ndi mdima. Mulungu adaona kuti zinali zabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 kuti zilamulire usana ndi usiku, ndi kuti zilekanitse kuwala ndi mdima. Mulungu anaona kuti zinali bwino. Onani mutuwo |