Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 1:17 - Buku Lopatulika

17 Mulungu ndipo adaika zimenezo m'thambo la kumwamba, kuti ziunikire padziko lapansi,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Mulungu ndipo adaika zimenezo m'thambo la kumwamba, kuti ziunikire pa dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Mulungu adaika miyuniyo ku thambo, kuti iziwunikira dziko lapansi,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Mulungu anaziyika mlengalenga kuti ziziwunikira pa dziko lapansi,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 1:17
7 Mawu Ofanana  

ndiika utawaleza wanga m'mtambomo, ndipo udzakhala chizindikiro cha pangano lopangana ndi Ine ndi dziko lapansi.


Kodi walamulira m'mawa chiyambire masiku ako, ndi kudziwitsa mbandakucha malo ake;


Yehova, Ambuye wathu, dzina lanu liposadi nanga padziko lonse lapansi! Inu amene munaika ulemerero wanu pa thambo la kumwamba.


Pakuona ine thambo la kumwamba lanu, ntchito ya zala zanu, mwezi ndi nyenyezi, zimene munazikhazika,


Pakuti Yehova atero: Ngati mukhoza kuswa pangano langa la usana ndi pangano langa la usiku, kuti usakhalenso usana ndi usiku, m'nyengo yao;


Yehova atero: Likaleka kukhala pangano langa la usana ndi usiku, ngati sindinalemba malemba a kumwamba ndi dziko lapansi;


Pakuti kotero anatilamula Ambuye ndi kuti, Ndakuika iwe kuunika kwa amitundu, kuti udzakhala iwe chipulumutso kufikira malekezero a dziko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa